Ndimadana nazo ine ndikamayandikila ku kagona kuchipinda nde wina azindiyimbila nthawi zino. Chabwino ndinu akunja koma kumawona nthawi zake zoyimba. Ine ndikamakuyimbilani ndimapanga book ma appointment ndi inu chifukwa aliyense amakhala ndizochita zambiri